Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 16 - طه - Page - Juz 16
﴿فَلَا يَصُدَّنَّكَ عَنۡهَا مَن لَّا يُؤۡمِنُ بِهَا وَٱتَّبَعَ هَوَىٰهُ فَتَرۡدَىٰ ﴾
[طه: 16]
﴿فلا يصدنك عنها من لا يؤمن بها واتبع هواه فتردى﴾ [طه: 16]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo asakutsekereze (ku khulupirira) zimenezo yemwe saikhulupirira (Kiyamayo), ndipo akungotsata zilakolako za mtima wake; kuopa kuti Ungadzaonongeke.” |