Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 5 - طه - Page - Juz 16
﴿ٱلرَّحۡمَٰنُ عَلَى ٱلۡعَرۡشِ ٱسۡتَوَىٰ ﴾
[طه: 5]
﴿الرحمن على العرش استوى﴾ [طه: 5]
Khaled Ibrahim Betala “(Iye ndi Allah), Wachifundo Chambiri; pa Arsh (Mpando wachifumu) adakhazikika, (kukhazikika koyenerana ndi ulemelero Wake kopanda kukufanizira ndi kukhazikika kwa chilichonse; pakuti Iye salingana ndi chilichonse pa chikhalidwe ndi mbiri Zake) |