Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 75 - طه - Page - Juz 16
﴿وَمَن يَأۡتِهِۦ مُؤۡمِنٗا قَدۡ عَمِلَ ٱلصَّٰلِحَٰتِ فَأُوْلَٰٓئِكَ لَهُمُ ٱلدَّرَجَٰتُ ٱلۡعُلَىٰ ﴾
[طه: 75]
﴿ومن يأته مؤمنا قد عمل الصالحات فأولئك لهم الدرجات العلا﴾ [طه: 75]
Khaled Ibrahim Betala “Koma amene adzamdzera uku ali wokhulupirira, yemwe adachita ntchito zabwino, iwo ndi amene adzapeze ulemewero wapamwamba |