×

Iye adati, “Ine ndidaona zimene iwo sanali kuona. Motero ine ndidatenga dothi 20:96 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ta-Ha ⮕ (20:96) ayat 96 in Chichewa

20:96 Surah Ta-Ha ayat 96 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 96 - طه - Page - Juz 16

﴿قَالَ بَصُرۡتُ بِمَا لَمۡ يَبۡصُرُواْ بِهِۦ فَقَبَضۡتُ قَبۡضَةٗ مِّنۡ أَثَرِ ٱلرَّسُولِ فَنَبَذۡتُهَا وَكَذَٰلِكَ سَوَّلَتۡ لِي نَفۡسِي ﴾
[طه: 96]

Iye adati, “Ine ndidaona zimene iwo sanali kuona. Motero ine ndidatenga dothi lodzala m’manja kuchokera ku fumbi lochokera ku phazi la Mtumwi ndi kulitaya. Kotero mzimu wanga udandikakamiza.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال بصرت بما لم يبصروا به فقبضت قبضة من أثر الرسول فنبذتها, باللغة نيانجا

﴿قال بصرت بما لم يبصروا به فقبضت قبضة من أثر الرسول فنبذتها﴾ [طه: 96]

Khaled Ibrahim Betala
“(Iye adati:) “Ndidaona zomwe sadazione (ena) ndipo ndidatapa pang’ono mapazi a Mtumiki (Gabriele) ndikuwaponya (mu fano la mwana wa ng’ombe). Ndipo zimenezi ndi zomwe zidakomera mtima wanga.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek