Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anbiya’ ayat 65 - الأنبيَاء - Page - Juz 17
﴿ثُمَّ نُكِسُواْ عَلَىٰ رُءُوسِهِمۡ لَقَدۡ عَلِمۡتَ مَا هَٰٓؤُلَآءِ يَنطِقُونَ ﴾
[الأنبيَاء: 65]
﴿ثم نكسوا على رءوسهم لقد علمت ما هؤلاء ينطقون﴾ [الأنبيَاء: 65]
Khaled Ibrahim Betala “Kenako adazyolitsa mitu yawo (ndikubwerera kuumbuli wawo) nanena kuti: “Ndithu iwe ukudziwa kuti izi siziyankhula (nchifukwa ninji ukutichita chipongwe)?” |