Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shu‘ara’ ayat 24 - الشعراء - Page - Juz 19
﴿قَالَ رَبُّ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِ وَمَا بَيۡنَهُمَآۖ إِن كُنتُم مُّوقِنِينَ ﴾
[الشعراء: 24]
﴿قال رب السموات والأرض وما بينهما إن كنتم موقنين﴾ [الشعراء: 24]
Khaled Ibrahim Betala “(Mûsa) adati: “Mbuye wa thambo ndi nthaka ndi zapakati pake, ngati muli ndi chitsimikizo. (Amachita chilichonse m’menemo mmene wafunira; kupereka moyo ndi imfa).” |