×

Patsiku limene chiweruzo chathu chidzayandikira kwa osakhulupirira, Ife tidzawabweretsera chinyama chimene chidzayankhula 27:82 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Naml ⮕ (27:82) ayat 82 in Chichewa

27:82 Surah An-Naml ayat 82 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Naml ayat 82 - النَّمل - Page - Juz 20

﴿۞ وَإِذَا وَقَعَ ٱلۡقَوۡلُ عَلَيۡهِمۡ أَخۡرَجۡنَا لَهُمۡ دَآبَّةٗ مِّنَ ٱلۡأَرۡضِ تُكَلِّمُهُمۡ أَنَّ ٱلنَّاسَ كَانُواْ بِـَٔايَٰتِنَا لَا يُوقِنُونَ ﴾
[النَّمل: 82]

Patsiku limene chiweruzo chathu chidzayandikira kwa osakhulupirira, Ife tidzawabweretsera chinyama chimene chidzayankhula nawo kuchokera ku dziko lapansi chifukwa munthu sanakhulupirire chivumbulutso chathu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا وقع القول عليهم أخرجنا لهم دابة من الأرض تكلمهم أن الناس, باللغة نيانجا

﴿وإذا وقع القول عليهم أخرجنا لهم دابة من الأرض تكلمهم أن الناس﴾ [النَّمل: 82]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo mawu (onena kudza kwa Qiyâma) akadzatsimikizika pa iwo, tidzawatulutsira chinyama m’nthaka chimene chidzawayankhula kuti ndithu anthu adalibe chitsimikizo pa Ayah (ndime) Zathu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek