×

Patsikulimeneli, lipengalidzalizidwandipoonseamene amakhala kumwamba ndi padziko lapansi adzagwidwa ndi mantha kupatula okhawo 27:87 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Naml ⮕ (27:87) ayat 87 in Chichewa

27:87 Surah An-Naml ayat 87 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Naml ayat 87 - النَّمل - Page - Juz 20

﴿وَيَوۡمَ يُنفَخُ فِي ٱلصُّورِ فَفَزِعَ مَن فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَمَن فِي ٱلۡأَرۡضِ إِلَّا مَن شَآءَ ٱللَّهُۚ وَكُلٌّ أَتَوۡهُ دَٰخِرِينَ ﴾
[النَّمل: 87]

Patsikulimeneli, lipengalidzalizidwandipoonseamene amakhala kumwamba ndi padziko lapansi adzagwidwa ndi mantha kupatula okhawo amene Mulungu adzafuna kuwapatula mu zimene zi. Onse adzabwera kwa Iye modzichepetsa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ويوم ينفخ في الصور ففزع من في السموات ومن في الأرض إلا, باللغة نيانجا

﴿ويوم ينفخ في الصور ففزع من في السموات ومن في الأرض إلا﴾ [النَّمل: 87]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (akumbutse za) tsiku limene lipenga (la chiweruziro) lidzaimbidwa, adzadzidzimuka amene ali kumwamba ndi amene ali pansi kupatula yemwe Allah wamfuna (kuti adzadzidzimuke); ndipo onse adzamdzera (Allah) ali odzichepetsa (ofooka)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek