Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 16 - القَصَص - Page - Juz 20
﴿قَالَ رَبِّ إِنِّي ظَلَمۡتُ نَفۡسِي فَٱغۡفِرۡ لِي فَغَفَرَ لَهُۥٓۚ إِنَّهُۥ هُوَ ٱلۡغَفُورُ ٱلرَّحِيمُ ﴾
[القَصَص: 16]
﴿قال رب إني ظلمت نفسي فاغفر لي فغفر له إنه هو الغفور﴾ [القَصَص: 16]
Khaled Ibrahim Betala “Adati: “E Mbuye wanga! Ndithu ndadzichitira zoipa ndekha! Choncho ndikhululukireni!” Tero (Allah) adamkhululukira (chifukwa sadalinge kupha). Ndithu Iye (Allah) Ngokhululuka, Ngwachisoni chosatha |