Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 34 - القَصَص - Page - Juz 20
﴿وَأَخِي هَٰرُونُ هُوَ أَفۡصَحُ مِنِّي لِسَانٗا فَأَرۡسِلۡهُ مَعِيَ رِدۡءٗا يُصَدِّقُنِيٓۖ إِنِّيٓ أَخَافُ أَن يُكَذِّبُونِ ﴾
[القَصَص: 34]
﴿وأخي هارون هو أفصح مني لسانا فأرسله معي ردءا يصدقني إني أخاف﴾ [القَصَص: 34]
Khaled Ibrahim Betala ““Ndipo m’bale wanga (Haaruni) ndikatswiri pakuyankhula kuposa ine. Mutumizeni pamodzi ndi ine monga mnthandizi, azikandivomereza (pa zimene ndizikanena). Ndithu ine ndikuopa kuti akanditsutsa.” |