×

Kotero Ife tidalamulira nthaka kuti imumeze Karuni pamodzi ndi chuma chake ndipo 28:81 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:81) ayat 81 in Chichewa

28:81 Surah Al-Qasas ayat 81 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 81 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿فَخَسَفۡنَا بِهِۦ وَبِدَارِهِ ٱلۡأَرۡضَ فَمَا كَانَ لَهُۥ مِن فِئَةٖ يَنصُرُونَهُۥ مِن دُونِ ٱللَّهِ وَمَا كَانَ مِنَ ٱلۡمُنتَصِرِينَ ﴾
[القَصَص: 81]

Kotero Ife tidalamulira nthaka kuti imumeze Karuni pamodzi ndi chuma chake ndipo sadapeze wina womuthandiza kwa Mulungu ndipo iye sadathe kudziteteza

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فخسفنا به وبداره الأرض فما كان له من فئة ينصرونه من دون, باللغة نيانجا

﴿فخسفنا به وبداره الأرض فما كان له من فئة ينصرونه من دون﴾ [القَصَص: 81]

Khaled Ibrahim Betala
“Kenako tidamdidimiza m’nthaka iye ndi nyumba yake; ndipo adalibe gulu lililonse lomuthangata popikisana ndi Allah, ndipo sadali mwa odzipulumutsa okha
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek