×

Kodi anthu amaganiza kuti adzasiyidwa okha osayesedwa chifukwa anena kuti, “Ife ndife 29:2 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:2) ayat 2 in Chichewa

29:2 Surah Al-‘Ankabut ayat 2 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 2 - العَنكبُوت - Page - Juz 20

﴿أَحَسِبَ ٱلنَّاسُ أَن يُتۡرَكُوٓاْ أَن يَقُولُوٓاْ ءَامَنَّا وَهُمۡ لَا يُفۡتَنُونَ ﴾
[العَنكبُوت: 2]

Kodi anthu amaganiza kuti adzasiyidwa okha osayesedwa chifukwa anena kuti, “Ife ndife okhulupirira?”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أحسب الناس أن يتركوا أن يقولوا آمنا وهم لا يفتنون, باللغة نيانجا

﴿أحسب الناس أن يتركوا أن يقولوا آمنا وهم لا يفتنون﴾ [العَنكبُوت: 2]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi anthu akuganiza kuti adzasiyidwa popanda kuyesedwa ndi masautso pakungonena kuti: “Takhulupirira?” (Iyayi, ayenera kuyesedwa ndithu ndi masautso osiyanasiyana pa matupi pawo ndi pachuma chawo kuti adziwike woona ndi wachiphamaso)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek