×

Ndipo musatsutsane ndi anthu okhulupirira za m’Buku pokhapokha kutakhala koyenera kutero, kupatula 29:46 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:46) ayat 46 in Chichewa

29:46 Surah Al-‘Ankabut ayat 46 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 46 - العَنكبُوت - Page - Juz 21

﴿۞ وَلَا تُجَٰدِلُوٓاْ أَهۡلَ ٱلۡكِتَٰبِ إِلَّا بِٱلَّتِي هِيَ أَحۡسَنُ إِلَّا ٱلَّذِينَ ظَلَمُواْ مِنۡهُمۡۖ وَقُولُوٓاْ ءَامَنَّا بِٱلَّذِيٓ أُنزِلَ إِلَيۡنَا وَأُنزِلَ إِلَيۡكُمۡ وَإِلَٰهُنَا وَإِلَٰهُكُمۡ وَٰحِدٞ وَنَحۡنُ لَهُۥ مُسۡلِمُونَ ﴾
[العَنكبُوت: 46]

Ndipo musatsutsane ndi anthu okhulupirira za m’Buku pokhapokha kutakhala koyenera kutero, kupatula okhawo amene amachita zoipa. Nena, “Ife timakhulupirira mu izo zimene zavumbulutsidwa kwa ife ndi zimene zidavumbulutsidwa kwa inu ndipo Mulungu wathu ndi Mulungu wanu ndi mmodzi ndipo ife tadzipereka kwa Iye.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولا تجادلوا أهل الكتاب إلا بالتي هي أحسن إلا الذين ظلموا منهم, باللغة نيانجا

﴿ولا تجادلوا أهل الكتاب إلا بالتي هي أحسن إلا الذين ظلموا منهم﴾ [العَنكبُوت: 46]

Khaled Ibrahim Betala
“۞ Ndipo musatsutsane ndi anthu a buku koma kutsutsana kwabwino kupatula amene achita zoipa mwa iwo. Ndipo nenani: “Takhulupirira zomwe zavumbulutsidwa kwa ife ndi zomwe zavumbulutsidwa kwa inu, ndipo Mulungu wathu ndi Mulungu wanu ndi Mmodzi; ndipo ife ndife ogonjera Iye.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek