×

Ndipokotero Ifetavumbulutsa Bukulolemekezekakwa iwe. Kotero onse amene tawapatsa Buku amakhulupirira mwa ilo 29:47 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:47) ayat 47 in Chichewa

29:47 Surah Al-‘Ankabut ayat 47 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 47 - العَنكبُوت - Page - Juz 21

﴿وَكَذَٰلِكَ أَنزَلۡنَآ إِلَيۡكَ ٱلۡكِتَٰبَۚ فَٱلَّذِينَ ءَاتَيۡنَٰهُمُ ٱلۡكِتَٰبَ يُؤۡمِنُونَ بِهِۦۖ وَمِنۡ هَٰٓؤُلَآءِ مَن يُؤۡمِنُ بِهِۦۚ وَمَا يَجۡحَدُ بِـَٔايَٰتِنَآ إِلَّا ٱلۡكَٰفِرُونَ ﴾
[العَنكبُوت: 47]

Ndipokotero Ifetavumbulutsa Bukulolemekezekakwa iwe. Kotero onse amene tawapatsa Buku amakhulupirira mwa ilo ndipo palibe amene amakana chivumbulutso chathu kupatula anthu osalungama

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وكذلك أنـزلنا إليك الكتاب فالذين آتيناهم الكتاب يؤمنون به ومن هؤلاء من, باللغة نيانجا

﴿وكذلك أنـزلنا إليك الكتاب فالذين آتيناهم الكتاب يؤمنون به ومن هؤلاء من﴾ [العَنكبُوت: 47]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo umo ndimomwe takuvumbulutsira buku (ili la Qur’an). Choncho amene tidawapatsa buku, (ili lisadadze, monga Taurat ndi Injili), akulikhulupirira; akulikhulupiriranso ena mwa awa (Arabu omwe sitidawapatse buku). Ndipo sangawakane ma Ayah Athu kupatula osakhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek