×

oh inu akapolo anga amene mwakhulupirira! Ndithudi dziko langa lili ndi malo 29:56 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:56) ayat 56 in Chichewa

29:56 Surah Al-‘Ankabut ayat 56 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 56 - العَنكبُوت - Page - Juz 21

﴿يَٰعِبَادِيَ ٱلَّذِينَ ءَامَنُوٓاْ إِنَّ أَرۡضِي وَٰسِعَةٞ فَإِيَّٰيَ فَٱعۡبُدُونِ ﴾
[العَنكبُوت: 56]

oh inu akapolo anga amene mwakhulupirira! Ndithudi dziko langa lili ndi malo ambiri. Kotero ndipembedzeni Ine ndekha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياعبادي الذين آمنوا إن أرضي واسعة فإياي فاعبدون, باللغة نيانجا

﴿ياعبادي الذين آمنوا إن أرضي واسعة فإياي فاعبدون﴾ [العَنكبُوت: 56]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu akapolo Anga amene mwakhulupirira! Ndithu nthaka Yanga njophanuka; (mukhoza kupita dziko lina ngati m’dziko lanulo simukupeza mwayi wopembedza Allah mokwanira); ndipo Ine ndekha ndipembedzeni
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek