×

Kodi iwo saona kuti tateteza malo odalitsika pamene anthu ena ali kutengedwa 29:67 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:67) ayat 67 in Chichewa

29:67 Surah Al-‘Ankabut ayat 67 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 67 - العَنكبُوت - Page - Juz 21

﴿أَوَلَمۡ يَرَوۡاْ أَنَّا جَعَلۡنَا حَرَمًا ءَامِنٗا وَيُتَخَطَّفُ ٱلنَّاسُ مِنۡ حَوۡلِهِمۡۚ أَفَبِٱلۡبَٰطِلِ يُؤۡمِنُونَ وَبِنِعۡمَةِ ٱللَّهِ يَكۡفُرُونَ ﴾
[العَنكبُوت: 67]

Kodi iwo saona kuti tateteza malo odalitsika pamene anthu ena ali kutengedwa mwankhanza pa malo owazungulira? Kodi iwo adzakhala ali kukhulupirirabe zabodza ndi kukana ubwino wa Mulungu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أو لم يروا أنا جعلنا حرما آمنا ويتخطف الناس من حولهم أفبالباطل, باللغة نيانجا

﴿أو لم يروا أنا جعلنا حرما آمنا ويتخطف الناس من حولهم أفبالباطل﴾ [العَنكبُوت: 67]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi saona kuti dziko lawo (mzinda wa Makka) talichita kukhala lopatulika, lamtendere pomwe anthu ena akutsompholedwa m’mphepete mwawo? Kodi akukhulupirira zachabe ndi kuukana mtendere wa Allah
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek