×

Kodi woipitsitsa ndani kuposa munthu amene amapeka bodza lokhudza Mulungu kapena amene 29:68 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:68) ayat 68 in Chichewa

29:68 Surah Al-‘Ankabut ayat 68 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 68 - العَنكبُوت - Page - Juz 21

﴿وَمَنۡ أَظۡلَمُ مِمَّنِ ٱفۡتَرَىٰ عَلَى ٱللَّهِ كَذِبًا أَوۡ كَذَّبَ بِٱلۡحَقِّ لَمَّا جَآءَهُۥٓۚ أَلَيۡسَ فِي جَهَنَّمَ مَثۡوٗى لِّلۡكَٰفِرِينَ ﴾
[العَنكبُوت: 68]

Kodi woipitsitsa ndani kuposa munthu amene amapeka bodza lokhudza Mulungu kapena amene amati choonadi ndi chabodza pamene auzidwa za icho? Kodi Gahena siidzakhala malo okhalamo anthu onse osakhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ومن أظلم ممن افترى على الله كذبا أو كذب بالحق لما جاءه, باللغة نيانجا

﴿ومن أظلم ممن افترى على الله كذبا أو كذب بالحق لما جاءه﴾ [العَنكبُوت: 68]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi wachinyengo wamkulu ndani woposa amene akupekera bodza Allah, kapena kutsutsa choona chikamdzera? Kodi si mu Jahannam momwe mudzakhala malo a osakhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek