×

Kotero dziperekeni kwathunthu ku chipembedzo choona lisanadze tsiku loopsa kuchokera kwa Mulungu 30:43 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ar-Rum ⮕ (30:43) ayat 43 in Chichewa

30:43 Surah Ar-Rum ayat 43 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Rum ayat 43 - الرُّوم - Page - Juz 21

﴿فَأَقِمۡ وَجۡهَكَ لِلدِّينِ ٱلۡقَيِّمِ مِن قَبۡلِ أَن يَأۡتِيَ يَوۡمٞ لَّا مَرَدَّ لَهُۥ مِنَ ٱللَّهِۖ يَوۡمَئِذٖ يَصَّدَّعُونَ ﴾
[الرُّوم: 43]

Kotero dziperekeni kwathunthu ku chipembedzo choona lisanadze tsiku loopsa kuchokera kwa Mulungu limene silidzatheka kulizemba. Pa tsiku limeneli anthu adzagawidwa m’magulu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فأقم وجهك للدين القيم من قبل أن يأتي يوم لا مرد له, باللغة نيانجا

﴿فأقم وجهك للدين القيم من قبل أن يأتي يوم لا مرد له﴾ [الرُّوم: 43]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho lunjika nkhope yako ku chipembedzo choongoka lisadadze tsiku losabwezedwa lochokera kwa Allah. Tsiku limenelo (anthu) adzagawikana, (abwino akalowa ku Munda wamtendere, pomwe oipa akalowa ku Moto)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek