Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Rum ayat 44 - الرُّوم - Page - Juz 21
﴿مَن كَفَرَ فَعَلَيۡهِ كُفۡرُهُۥۖ وَمَنۡ عَمِلَ صَٰلِحٗا فَلِأَنفُسِهِمۡ يَمۡهَدُونَ ﴾
[الرُّوم: 44]
﴿من كفر فعليه كفره ومن عمل صالحا فلأنفسهم يمهدون﴾ [الرُّوم: 44]
Khaled Ibrahim Betala “Amene sanakhulupirire, kuipa kwa kusakhulupirira kwake kuli pa iye (mwini). Ndipo amene achita zabwino iwo akudzikonzera okha (zabwino) |