Quran with Chichewa translation - Surah As-Sajdah ayat 26 - السَّجدة - Page - Juz 21
﴿أَوَلَمۡ يَهۡدِ لَهُمۡ كَمۡ أَهۡلَكۡنَا مِن قَبۡلِهِم مِّنَ ٱلۡقُرُونِ يَمۡشُونَ فِي مَسَٰكِنِهِمۡۚ إِنَّ فِي ذَٰلِكَ لَأٓيَٰتٍۚ أَفَلَا يَسۡمَعُونَ ﴾
[السَّجدة: 26]
﴿أو لم يهد لهم كم أهلكنا من قبلهم من القرون يمشون في﴾ [السَّجدة: 26]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi sizidadziwike kwa iwo kuti ndimibadwo ingati imene tidaiononga patsogolo pawo; (chikhalirecho iwo) akudutsa mokhala mwawo? Ndithu m’zimenezo, muli zizindikiro, kodi sakumva |