Quran with Chichewa translation - Surah As-Sajdah ayat 3 - السَّجدة - Page - Juz 21
﴿أَمۡ يَقُولُونَ ٱفۡتَرَىٰهُۚ بَلۡ هُوَ ٱلۡحَقُّ مِن رَّبِّكَ لِتُنذِرَ قَوۡمٗا مَّآ أَتَىٰهُم مِّن نَّذِيرٖ مِّن قَبۡلِكَ لَعَلَّهُمۡ يَهۡتَدُونَ ﴾
[السَّجدة: 3]
﴿أم يقولون افتراه بل هو الحق من ربك لتنذر قوما ما أتاهم﴾ [السَّجدة: 3]
Khaled Ibrahim Betala “Kapena akunena kuti: “Walipeka yekha (bukulo)?” Iyayi, ichi nchoona chimene chachokera kwa Mbuye wako kuti uwachenjeze anthu ndi chimenechi, amene sadawadzere mchenjezi iwe usadadze. Kuti aongoke (ndi kutsatira njira yolungama) |