×

Ndipo anthu a m’Buku amene adawathandiza iwo, Mulungu adawachotsa kumalo awo okhazikika 33:26 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:26) ayat 26 in Chichewa

33:26 Surah Al-Ahzab ayat 26 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 26 - الأحزَاب - Page - Juz 21

﴿وَأَنزَلَ ٱلَّذِينَ ظَٰهَرُوهُم مِّنۡ أَهۡلِ ٱلۡكِتَٰبِ مِن صَيَاصِيهِمۡ وَقَذَفَ فِي قُلُوبِهِمُ ٱلرُّعۡبَ فَرِيقٗا تَقۡتُلُونَ وَتَأۡسِرُونَ فَرِيقٗا ﴾
[الأحزَاب: 26]

Ndipo anthu a m’Buku amene adawathandiza iwo, Mulungu adawachotsa kumalo awo okhazikika ndipo adakhazika mantha m’mitima mwawo, kotero inu mudapha ena ndi ena mudawagwira ukapolo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وأنـزل الذين ظاهروهم من أهل الكتاب من صياصيهم وقذف في قلوبهم الرعب, باللغة نيانجا

﴿وأنـزل الذين ظاهروهم من أهل الكتاب من صياصيهم وقذف في قلوبهم الرعب﴾ [الأحزَاب: 26]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo adawatsitsa m’malinga mwawo amene adathandiza adaniwo mwa anthu a buku (Ayuda). Ndipo adathira mantha m’mitima mwawo. Ena mumawapha; ndipo ena mumawagwira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek