×

Iwo amene amalalikira uthenga wa Mulungu ndipo amene amamuopa Iye, iwo saopa 33:39 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:39) ayat 39 in Chichewa

33:39 Surah Al-Ahzab ayat 39 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 39 - الأحزَاب - Page - Juz 22

﴿ٱلَّذِينَ يُبَلِّغُونَ رِسَٰلَٰتِ ٱللَّهِ وَيَخۡشَوۡنَهُۥ وَلَا يَخۡشَوۡنَ أَحَدًا إِلَّا ٱللَّهَۗ وَكَفَىٰ بِٱللَّهِ حَسِيبٗا ﴾
[الأحزَاب: 39]

Iwo amene amalalikira uthenga wa Mulungu ndipo amene amamuopa Iye, iwo saopa wina aliyense koma Mulungu ndipo Mulungu ndi wokwanira kubwezera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: الذين يبلغون رسالات الله ويخشونه ولا يخشون أحدا إلا الله وكفى بالله, باللغة نيانجا

﴿الذين يبلغون رسالات الله ويخشونه ولا يخشون أحدا إلا الله وكفى بالله﴾ [الأحزَاب: 39]

Khaled Ibrahim Betala
“(Aneneri) amene amafikitsa uthenga wa Allah (kwa anthu) uku akumuopa Iye, ndipo samamuopa aliyense koma Allah (yekha). Ndipo Allah Akukwana kukhala wowerengera (zochita za akapolo Ake)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek