×

Palibe vuto kwa Mtumwi pa zimene Mulungu wamupatsa ngati udindo wake. Chidali 33:38 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:38) ayat 38 in Chichewa

33:38 Surah Al-Ahzab ayat 38 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 38 - الأحزَاب - Page - Juz 22

﴿مَّا كَانَ عَلَى ٱلنَّبِيِّ مِنۡ حَرَجٖ فِيمَا فَرَضَ ٱللَّهُ لَهُۥۖ سُنَّةَ ٱللَّهِ فِي ٱلَّذِينَ خَلَوۡاْ مِن قَبۡلُۚ وَكَانَ أَمۡرُ ٱللَّهِ قَدَرٗا مَّقۡدُورًا ﴾
[الأحزَاب: 38]

Palibe vuto kwa Mtumwi pa zimene Mulungu wamupatsa ngati udindo wake. Chidali chizolowezi cha Mulungu kwa anthu amene adalipo kale. Ndipo ulamuliro wa Mulungu ndi wokhazikika

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ما كان على النبي من حرج فيما فرض الله له سنة الله, باللغة نيانجا

﴿ما كان على النبي من حرج فيما فرض الله له سنة الله﴾ [الأحزَاب: 38]

Khaled Ibrahim Betala
“Palibe tchimo pa Mneneri pa zimene Allah wamulamula. Chimenechi ndichizolowezi cha Allah (njira ya Allah) pa amene adanka kale. Ndipo lamulo la Allah ndi chikonzero (chomwe) chidakonzedwa. (Ndipo sichisinthidwa)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek