×

Ngati anthu achinyengo pamodzi ndi iwo amene m’mitima mwawo muli matenda ndiponso 33:60 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:60) ayat 60 in Chichewa

33:60 Surah Al-Ahzab ayat 60 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 60 - الأحزَاب - Page - Juz 22

﴿۞ لَّئِن لَّمۡ يَنتَهِ ٱلۡمُنَٰفِقُونَ وَٱلَّذِينَ فِي قُلُوبِهِم مَّرَضٞ وَٱلۡمُرۡجِفُونَ فِي ٱلۡمَدِينَةِ لَنُغۡرِيَنَّكَ بِهِمۡ ثُمَّ لَا يُجَاوِرُونَكَ فِيهَآ إِلَّا قَلِيلٗا ﴾
[الأحزَاب: 60]

Ngati anthu achinyengo pamodzi ndi iwo amene m’mitima mwawo muli matenda ndiponso anthu amene amayambitsa chisokonezo mu mzinda, saleka mchitidwe oterewu,** ndithudi, Ife tidzalimbana nawo ndipo iwo sadzakhala pafupi ndi inu kupatula nthawi yochepa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لئن لم ينته المنافقون والذين في قلوبهم مرض والمرجفون في المدينة لنغرينك, باللغة نيانجا

﴿لئن لم ينته المنافقون والذين في قلوبهم مرض والمرجفون في المدينة لنغرينك﴾ [الأحزَاب: 60]

Khaled Ibrahim Betala
“Ngati sasiya (machitidwe awo oipa) achiphamaso (achinyengo), ndi amene m’mitima mwawo muli matenda (a chiwerewere), ndi ofalitsa mbiri zoipa mu mzinda, tikukhwirizira kwa iwo (kuti uwathire nkhondo). Kenako sadzakhala m’menemo pamodzi ndi iwe, koma nthawi yochepa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek