Quran with Chichewa translation - Surah Saba’ ayat 2 - سَبإ - Page - Juz 22
﴿يَعۡلَمُ مَا يَلِجُ فِي ٱلۡأَرۡضِ وَمَا يَخۡرُجُ مِنۡهَا وَمَا يَنزِلُ مِنَ ٱلسَّمَآءِ وَمَا يَعۡرُجُ فِيهَاۚ وَهُوَ ٱلرَّحِيمُ ٱلۡغَفُورُ ﴾
[سَبإ: 2]
﴿يعلم ما يلج في الأرض وما يخرج منها وما ينـزل من السماء﴾ [سَبإ: 2]
Khaled Ibrahim Betala “Akudziwa zimene zikulowa m’nthaka ndi zimene zikutulukamo; ndi zimene zikutsika kumwamba ndi zimene zikukwera kumeneko. Ndipo Iye Ngwachifundo kwabasi, Ngokhululuka kwambiri |