Quran with Chichewa translation - Surah Saba’ ayat 21 - سَبإ - Page - Juz 22
﴿وَمَا كَانَ لَهُۥ عَلَيۡهِم مِّن سُلۡطَٰنٍ إِلَّا لِنَعۡلَمَ مَن يُؤۡمِنُ بِٱلۡأٓخِرَةِ مِمَّنۡ هُوَ مِنۡهَا فِي شَكّٖۗ وَرَبُّكَ عَلَىٰ كُلِّ شَيۡءٍ حَفِيظٞ ﴾
[سَبإ: 21]
﴿وما كان له عليهم من سلطان إلا لنعلم من يؤمن بالآخرة ممن﴾ [سَبإ: 21]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo iye adalibe nyonga pa iwo, koma chifukwa chakuti tionetse poyera ndani wokhulupirira tsiku la chimaliziro ndiponso ndani amene akulikaikira. Ndipo Mbuye wako Ngosunga chilichonse |