Quran with Chichewa translation - Surah Saba’ ayat 48 - سَبإ - Page - Juz 22
﴿قُلۡ إِنَّ رَبِّي يَقۡذِفُ بِٱلۡحَقِّ عَلَّٰمُ ٱلۡغُيُوبِ ﴾
[سَبإ: 48]
﴿قل إن ربي يقذف بالحق علام الغيوب﴾ [سَبإ: 48]
Khaled Ibrahim Betala “Nena: “Ndithu Mbuye wanga amaponya choonadi (ponseponse kotero kuti chonama chimathawa). Ngodziwa zedi (zinthu) zobisika.” |