Quran with Chichewa translation - Surah Saba’ ayat 49 - سَبإ - Page - Juz 22
﴿قُلۡ جَآءَ ٱلۡحَقُّ وَمَا يُبۡدِئُ ٱلۡبَٰطِلُ وَمَا يُعِيدُ ﴾
[سَبإ: 49]
﴿قل جاء الحق وما يبدئ الباطل وما يعيد﴾ [سَبإ: 49]
Khaled Ibrahim Betala “Nena: “Choonadi chadza (chisilamu); ndipo chabodza (chipembedzo cha mafano) sichidzetsa zachilendo, ndiponso sichibwerera (kukhala ndi nyonga monga kale).” |