×

Nena, “Malipiro ena aliwonse amene ndidakufunsani ndi anu chifukwa malipiro anga ali 34:47 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Saba’ ⮕ (34:47) ayat 47 in Chichewa

34:47 Surah Saba’ ayat 47 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Saba’ ayat 47 - سَبإ - Page - Juz 22

﴿قُلۡ مَا سَأَلۡتُكُم مِّنۡ أَجۡرٖ فَهُوَ لَكُمۡۖ إِنۡ أَجۡرِيَ إِلَّا عَلَى ٱللَّهِۖ وَهُوَ عَلَىٰ كُلِّ شَيۡءٖ شَهِيدٞ ﴾
[سَبإ: 47]

Nena, “Malipiro ena aliwonse amene ndidakufunsani ndi anu chifukwa malipiro anga ali ndi Mulungu ndipo Iye ndi mboni pa zinthu zonse.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل ما سألتكم من أجر فهو لكم إن أجري إلا على الله, باللغة نيانجا

﴿قل ما سألتكم من أجر فهو لكم إن أجري إلا على الله﴾ [سَبإ: 47]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Chilichonse ndakupemphani kukhala malipiro (othandizira kufikitsa uthenga kwa anthu) ndichanu, malipiro anga ali kwa Allah basi. Ndipo Iye ndi Mboni pachilichonse.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek