×

Ndipo ngati iwo akuti iwe ndiwe wabodza, nawonso amene adalipo kale, adawatcha 35:25 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah FaTir ⮕ (35:25) ayat 25 in Chichewa

35:25 Surah FaTir ayat 25 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 25 - فَاطِر - Page - Juz 22

﴿وَإِن يُكَذِّبُوكَ فَقَدۡ كَذَّبَ ٱلَّذِينَ مِن قَبۡلِهِمۡ جَآءَتۡهُمۡ رُسُلُهُم بِٱلۡبَيِّنَٰتِ وَبِٱلزُّبُرِ وَبِٱلۡكِتَٰبِ ٱلۡمُنِيرِ ﴾
[فَاطِر: 25]

Ndipo ngati iwo akuti iwe ndiwe wabodza, nawonso amene adalipo kale, adawatcha Atumwi awo kuti ndi abodza. Atumwi awo adadza kwa iwo ndi chiphunzitso chomveka ndi mawu opatulika ndi Buku la muuni

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإن يكذبوك فقد كذب الذين من قبلهم جاءتهم رسلهم بالبينات وبالزبر وبالكتاب, باللغة نيانجا

﴿وإن يكذبوك فقد كذب الذين من قبلهم جاءتهم رسلهم بالبينات وبالزبر وبالكتاب﴾ [فَاطِر: 25]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ngati angakutsutse (sichachilendo), ndithu amene adali patsogolo pawo adatsutsanso. Aneneri awo adawadzera ndi zizindikiro zoonekera poyera, ndi malemba ndi buku lounikira (njira yabwino)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek