×

Ndithudi Ife takutumiza iwe ndi choonadi ngati wotenga nkhani zabwino ndi mchenjezi 35:24 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah FaTir ⮕ (35:24) ayat 24 in Chichewa

35:24 Surah FaTir ayat 24 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 24 - فَاطِر - Page - Juz 22

﴿إِنَّآ أَرۡسَلۡنَٰكَ بِٱلۡحَقِّ بَشِيرٗا وَنَذِيرٗاۚ وَإِن مِّنۡ أُمَّةٍ إِلَّا خَلَا فِيهَا نَذِيرٞ ﴾
[فَاطِر: 24]

Ndithudi Ife takutumiza iwe ndi choonadi ngati wotenga nkhani zabwino ndi mchenjezi ndipo palibe mtundu wa anthu umene sadakhale ndi mchenjezi pakati pawo kalelo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إنا أرسلناك بالحق بشيرا ونذيرا وإن من أمة إلا خلا فيها نذير, باللغة نيانجا

﴿إنا أرسلناك بالحق بشيرا ونذيرا وإن من أمة إلا خلا فيها نذير﴾ [فَاطِر: 24]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu Ife takutuma mwachoona kuti unene nkhani yabwino (yokalowa ku Munda wamtendere kwa amene akhulupirira), ndi kuti uchenjeze (za chilango cha Moto kwa amene sadakhulupirire). Ndipo palibe m’badwo uliwonse koma mchenjezi adapitamo
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek