Quran with Chichewa translation - Surah As-saffat ayat 37 - الصَّافَات - Page - Juz 23
﴿بَلۡ جَآءَ بِٱلۡحَقِّ وَصَدَّقَ ٱلۡمُرۡسَلِينَ ﴾
[الصَّافَات: 37]
﴿بل جاء بالحق وصدق المرسلين﴾ [الصَّافَات: 37]
Khaled Ibrahim Betala “Iyayi koma adawadzera ndi choonadi (Mthenga wawo Muhammad yemwe siwamisala kapena wolakatula zopeka) ndipo adawatsimikizira za atumiki |