×

Kapena iwo ali ndi ulamuliro kumwamba ndi padziko ndi kuti zonse zimene 38:10 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah sad ⮕ (38:10) ayat 10 in Chichewa

38:10 Surah sad ayat 10 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 10 - صٓ - Page - Juz 23

﴿أَمۡ لَهُم مُّلۡكُ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِ وَمَا بَيۡنَهُمَاۖ فَلۡيَرۡتَقُواْ فِي ٱلۡأَسۡبَٰبِ ﴾
[صٓ: 10]

Kapena iwo ali ndi ulamuliro kumwamba ndi padziko ndi kuti zonse zimene zili m’menemo ndi zawo? Ngati nditero, alekeni iwo kuti akwere mothandizidwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أم لهم ملك السموات والأرض وما بينهما فليرتقوا في الأسباب, باللغة نيانجا

﴿أم لهم ملك السموات والأرض وما بينهما فليرتقوا في الأسباب﴾ [صٓ: 10]

Khaled Ibrahim Betala
“Kapena ufumu wa kumwamba ndi pansi ndi zapakati pake, ngwawo. Ngati zili choncho atakwera makwelero (kuti akafike pamalo poti akalamulire zimene akufuna, ngati angathe kutero)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek