Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 11 - صٓ - Page - Juz 23
﴿جُندٞ مَّا هُنَالِكَ مَهۡزُومٞ مِّنَ ٱلۡأَحۡزَابِ ﴾
[صٓ: 11]
﴿جند ما هنالك مهزوم من الأحزاب﴾ [صٓ: 11]
Khaled Ibrahim Betala “Awa (Aquraish kuonjezera pa kudzitama kwawo), nkagulu kochepa ndi kofooka. Kagonjetsedwa monga makamu ankhondo (omwe adagonjetsedwa kale omwe amatsutsana ndi aneneri akale) |