Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 29 - صٓ - Page - Juz 23
﴿كِتَٰبٌ أَنزَلۡنَٰهُ إِلَيۡكَ مُبَٰرَكٞ لِّيَدَّبَّرُوٓاْ ءَايَٰتِهِۦ وَلِيَتَذَكَّرَ أُوْلُواْ ٱلۡأَلۡبَٰبِ ﴾
[صٓ: 29]
﴿كتاب أنـزلناه إليك مبارك ليدبروا آياته وليتذكر أولو الألباب﴾ [صٓ: 29]
Khaled Ibrahim Betala “(Ili), ndibuku lochuluka madalitso lomwe talivumbulutsa kwa iwe kuti (anthu) azame kwambiri pomvetsetsa ndime zake; ndi kuti apeze nalo phunziro eni nzeru |