×

Kodi Ife tingasamale mofanana anthu okhulupirira ndi ochita ntchito zabwino ndi iwo 38:28 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah sad ⮕ (38:28) ayat 28 in Chichewa

38:28 Surah sad ayat 28 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 28 - صٓ - Page - Juz 23

﴿أَمۡ نَجۡعَلُ ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَعَمِلُواْ ٱلصَّٰلِحَٰتِ كَٱلۡمُفۡسِدِينَ فِي ٱلۡأَرۡضِ أَمۡ نَجۡعَلُ ٱلۡمُتَّقِينَ كَٱلۡفُجَّارِ ﴾
[صٓ: 28]

Kodi Ife tingasamale mofanana anthu okhulupirira ndi ochita ntchito zabwino ndi iwo amene amadzetsa chisokonezo pa dziko? Kapena Ife tingasamalire anthu amene amalewa zoipa chimodzimodzi ndi iwo amene amachita zoipa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أم نجعل الذين آمنوا وعملوا الصالحات كالمفسدين في الأرض أم نجعل المتقين, باللغة نيانجا

﴿أم نجعل الذين آمنوا وعملوا الصالحات كالمفسدين في الأرض أم نجعل المتقين﴾ [صٓ: 28]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi tingawachite amene akhulupirira (Allah) ndi kuchita zabwino kukhala monga oononga pa dziko? Kapena tiwachite oopa (Allah) monga oipa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek