Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 30 - صٓ - Page - Juz 23
﴿وَوَهَبۡنَا لِدَاوُۥدَ سُلَيۡمَٰنَۚ نِعۡمَ ٱلۡعَبۡدُ إِنَّهُۥٓ أَوَّابٌ ﴾
[صٓ: 30]
﴿ووهبنا لداود سليمان نعم العبد إنه أواب﴾ [صٓ: 30]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo Daud tidampatsa (dalitso lobereka) Sulaiman, amene adali munthu wabwino. Ndithu iye adali wochulukitsa kutembenukira kwa Allah (ndi kudzichepetsa m’chikhalidwe chake chonse) |