Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 46 - صٓ - Page - Juz 23
﴿إِنَّآ أَخۡلَصۡنَٰهُم بِخَالِصَةٖ ذِكۡرَى ٱلدَّارِ ﴾ 
[صٓ: 46]
﴿إنا أخلصناهم بخالصة ذكرى الدار﴾ [صٓ: 46]
| Khaled Ibrahim Betala “Ndithu Ife tidawasankha powapatsa chikhalidwe chabwino (chomwe) ndi kukumbukira Nyumba yomaliza (nthawi zonse) |