×

Ndipo, ndithudi, ngati ungawafunse kuti, “Kodi ndani adalenga kumwamba ndi dziko lapansi?” 39:38 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:38) ayat 38 in Chichewa

39:38 Surah Az-Zumar ayat 38 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 38 - الزُّمَر - Page - Juz 24

﴿وَلَئِن سَأَلۡتَهُم مَّنۡ خَلَقَ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضَ لَيَقُولُنَّ ٱللَّهُۚ قُلۡ أَفَرَءَيۡتُم مَّا تَدۡعُونَ مِن دُونِ ٱللَّهِ إِنۡ أَرَادَنِيَ ٱللَّهُ بِضُرٍّ هَلۡ هُنَّ كَٰشِفَٰتُ ضُرِّهِۦٓ أَوۡ أَرَادَنِي بِرَحۡمَةٍ هَلۡ هُنَّ مُمۡسِكَٰتُ رَحۡمَتِهِۦۚ قُلۡ حَسۡبِيَ ٱللَّهُۖ عَلَيۡهِ يَتَوَكَّلُ ٱلۡمُتَوَكِّلُونَ ﴾
[الزُّمَر: 38]

Ndipo, ndithudi, ngati ungawafunse kuti, “Kodi ndani adalenga kumwamba ndi dziko lapansi?” Ndithudi iwo adzayankha kuti, “Ndi Mulungu.” Nena, “Kodi zinthu zimene mumapembedza m’malo mwa Mulungu, ngati Mulungu afuna kugwetsa mavuto pa ine, kodi zinthuzo zingathe kuchotsa mavutowo? Kapena ngati Iye alangiza chisomo chake pa ine, kodi izo zingakanize chisomo chake?” Nena, “Mulungu ndi wokwana kwa ine. Mwa Iye onse okhulupirira ayenera kuika chikhulupiriro chawo.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولئن سألتهم من خلق السموات والأرض ليقولن الله قل أفرأيتم ما تدعون, باللغة نيانجا

﴿ولئن سألتهم من خلق السموات والأرض ليقولن الله قل أفرأيتم ما تدعون﴾ [الزُّمَر: 38]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ukawafunsa (kuti) ndani adalenga thambo ndi nthaka, ndithu anena (kuti ndi) “Allah.” Nena: “Kodi mukuona bwanji, amene mukuwapembedza kusiya Allah angandichotsere masautso ake ngati Allah atafuna kundipatsa masautso? Kapena Allah atafuna kundichitira chifundo, kodi iwo angatsekereze chifundo Chakecho?” Nena: “Allah akundikwanira! Kwa Iye, atsamire otsamira.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek