Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 13 - النِّسَاء - Page - Juz 4
﴿تِلۡكَ حُدُودُ ٱللَّهِۚ وَمَن يُطِعِ ٱللَّهَ وَرَسُولَهُۥ يُدۡخِلۡهُ جَنَّٰتٖ تَجۡرِي مِن تَحۡتِهَا ٱلۡأَنۡهَٰرُ خَٰلِدِينَ فِيهَاۚ وَذَٰلِكَ ٱلۡفَوۡزُ ٱلۡعَظِيمُ ﴾
[النِّسَاء: 13]
﴿تلك حدود الله ومن يطع الله ورسوله يدخله جنات تجري من تحتها﴾ [النِّسَاء: 13]
Khaled Ibrahim Betala “Amenewo ndiwo malire a Allah; (musawalumphe). Ndipo amene angamvere Allah ndi Mtumiki Wake adzamulowetsa m’Minda yomwe pansi (ndi patsogolo pake) mitsinje ikuyenda. Adzakhala m’menemo nthawi yaitali. Kumeneko ndiko kupambana kwakukulu |