×

Koma iye amene amanyoza Mulungu ndi Mtumwi wake ndipo amalumpha malire ake, 4:14 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:14) ayat 14 in Chichewa

4:14 Surah An-Nisa’ ayat 14 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 14 - النِّسَاء - Page - Juz 4

﴿وَمَن يَعۡصِ ٱللَّهَ وَرَسُولَهُۥ وَيَتَعَدَّ حُدُودَهُۥ يُدۡخِلۡهُ نَارًا خَٰلِدٗا فِيهَا وَلَهُۥ عَذَابٞ مُّهِينٞ ﴾
[النِّسَاء: 14]

Koma iye amene amanyoza Mulungu ndi Mtumwi wake ndipo amalumpha malire ake, adzamuponya ku moto wa ku Gahena ndipo adzakhala komweko mpaka kalekale ndipo iye adzalandira chilango chochititsa manyazi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ومن يعص الله ورسوله ويتعد حدوده يدخله نارا خالدا فيها وله عذاب, باللغة نيانجا

﴿ومن يعص الله ورسوله ويتعد حدوده يدخله نارا خالدا فيها وله عذاب﴾ [النِّسَاء: 14]

Khaled Ibrahim Betala
“Koma amene anganyoze Allah ndi Mtumiki Wake, ndi kulumpha malire ake, (Allah) adzamulowetsa ku Moto; nadzakhala m’menemo nthawi yaitali. Ndipo adzapeza chilango chosambula
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek