×

Kupatula iwo amene alapa zoipa zawo ndi kuchita ntchito zabwino ndipo ayeretsa 4:146 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:146) ayat 146 in Chichewa

4:146 Surah An-Nisa’ ayat 146 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 146 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿إِلَّا ٱلَّذِينَ تَابُواْ وَأَصۡلَحُواْ وَٱعۡتَصَمُواْ بِٱللَّهِ وَأَخۡلَصُواْ دِينَهُمۡ لِلَّهِ فَأُوْلَٰٓئِكَ مَعَ ٱلۡمُؤۡمِنِينَۖ وَسَوۡفَ يُؤۡتِ ٱللَّهُ ٱلۡمُؤۡمِنِينَ أَجۡرًا عَظِيمٗا ﴾
[النِّسَاء: 146]

Kupatula iwo amene alapa zoipa zawo ndi kuchita ntchito zabwino ndipo ayeretsa chipembedzo chawo. Iwo adzakhala pamodzi ndi anthu okhulupirira. Ndipo Mulungu adzawapatsa anthu okhulupirira mphotho yaikulu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إلا الذين تابوا وأصلحوا واعتصموا بالله وأخلصوا دينهم لله فأولئك مع المؤمنين, باللغة نيانجا

﴿إلا الذين تابوا وأصلحوا واعتصموا بالله وأخلصوا دينهم لله فأولئك مع المؤمنين﴾ [النِّسَاء: 146]

Khaled Ibrahim Betala
“Kupatula amene alapa (pambuyo pa uchiphamaso wawo); nakonza (makhalidwe awo) nadziphatika kwa Allah; namuyeretseranso Allah chipembedzo chawo. Choncho iwo ali pamodzi ndi okhulupirira. Ndipo Allah adzapatsa okhulupirira malipiro akulu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek