×

Ndipo iwo, mwa akazi anu, amene achita chigololo, pezani mboni zokwanira zinayi 4:15 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:15) ayat 15 in Chichewa

4:15 Surah An-Nisa’ ayat 15 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 15 - النِّسَاء - Page - Juz 4

﴿وَٱلَّٰتِي يَأۡتِينَ ٱلۡفَٰحِشَةَ مِن نِّسَآئِكُمۡ فَٱسۡتَشۡهِدُواْ عَلَيۡهِنَّ أَرۡبَعَةٗ مِّنكُمۡۖ فَإِن شَهِدُواْ فَأَمۡسِكُوهُنَّ فِي ٱلۡبُيُوتِ حَتَّىٰ يَتَوَفَّىٰهُنَّ ٱلۡمَوۡتُ أَوۡ يَجۡعَلَ ٱللَّهُ لَهُنَّ سَبِيلٗا ﴾
[النِّسَاء: 15]

Ndipo iwo, mwa akazi anu, amene achita chigololo, pezani mboni zokwanira zinayi zochokera pakati panu ndipo ngati iwo apereka umboni wotsimikiza, asungeni kunyumba zawo mpaka pamene imfa iwapeza kapena mpaka pamene Mulungu alamula kwa iwo njira ina

❮ Previous Next ❯

ترجمة: واللاتي يأتين الفاحشة من نسائكم فاستشهدوا عليهن أربعة منكم فإن شهدوا فأمسكوهن, باللغة نيانجا

﴿واللاتي يأتين الفاحشة من نسائكم فاستشهدوا عليهن أربعة منكم فإن شهدوا فأمسكوهن﴾ [النِّسَاء: 15]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo omwe achite cha uve (chigololo) mwa akazi anu, afunireni mboni zinayi za mwa inu zoikira umboni pa iwo. Ngati ataikira umboni (kuti achitadi cha uvecho), atsekereni m’nyumba kufikira imfa idzawapeze, kapena Allah adzawaikire njira ina (monga kuphedwa)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek