×

Ndi kulandira kwawo kwa katapira pamene iwo ataletsedwa kutero, ndi kudya kwawo 4:161 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:161) ayat 161 in Chichewa

4:161 Surah An-Nisa’ ayat 161 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 161 - النِّسَاء - Page - Juz 6

﴿وَأَخۡذِهِمُ ٱلرِّبَوٰاْ وَقَدۡ نُهُواْ عَنۡهُ وَأَكۡلِهِمۡ أَمۡوَٰلَ ٱلنَّاسِ بِٱلۡبَٰطِلِۚ وَأَعۡتَدۡنَا لِلۡكَٰفِرِينَ مِنۡهُمۡ عَذَابًا أَلِيمٗا ﴾
[النِّسَاء: 161]

Ndi kulandira kwawo kwa katapira pamene iwo ataletsedwa kutero, ndi kudya kwawo kwa chuma cha anthu mwachinyengo. Ndipo Ife takonza chilango chowawa cha anthu osakhulupirira amene ali pakati pawo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وأخذهم الربا وقد نهوا عنه وأكلهم أموال الناس بالباطل وأعتدنا للكافرين منهم, باللغة نيانجا

﴿وأخذهم الربا وقد نهوا عنه وأكلهم أموال الناس بالباطل وأعتدنا للكافرين منهم﴾ [النِّسَاء: 161]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndi kudya kwawo riba (katapira) pomwe adaletsedwa kuti asadye; ndiponso chifukwa chakudya kwawo chuma cha anthu mwachinyengo. Ndipo osakhulupirira mwa iwo tawakonzera chilango chopweteka
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek