×

Motero iwo amene amakhulupirira mwa Mulungu ndipo amadzipereka kwathunthu kwa Iye, adzawalowetsa 4:175 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:175) ayat 175 in Chichewa

4:175 Surah An-Nisa’ ayat 175 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 175 - النِّسَاء - Page - Juz 6

﴿فَأَمَّا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ بِٱللَّهِ وَٱعۡتَصَمُواْ بِهِۦ فَسَيُدۡخِلُهُمۡ فِي رَحۡمَةٖ مِّنۡهُ وَفَضۡلٖ وَيَهۡدِيهِمۡ إِلَيۡهِ صِرَٰطٗا مُّسۡتَقِيمٗا ﴾
[النِّسَاء: 175]

Motero iwo amene amakhulupirira mwa Mulungu ndipo amadzipereka kwathunthu kwa Iye, adzawalowetsa ku chifundo ndi chisomo chake ndi kuwatsogolera kunjira yoyenera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فأما الذين آمنوا بالله واعتصموا به فسيدخلهم في رحمة منه وفضل ويهديهم, باللغة نيانجا

﴿فأما الذين آمنوا بالله واعتصموا به فسيدخلهم في رحمة منه وفضل ويهديهم﴾ [النِّسَاء: 175]

Khaled Ibrahim Betala
“Tsono amene akhulupirira Allah ndi kudziphatika kwa Iye, iwo adzawalowetsa ku chifundo ndi kuzabwino zochokera kwa Iye, ndikuwatsogolera kwa Iye njira yoongoka
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek