×

Pamene iwo amva nkhani iliyonse ya mtendere kapena yochititsa mantha, iwo amaiulutsa 4:83 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:83) ayat 83 in Chichewa

4:83 Surah An-Nisa’ ayat 83 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 83 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿وَإِذَا جَآءَهُمۡ أَمۡرٞ مِّنَ ٱلۡأَمۡنِ أَوِ ٱلۡخَوۡفِ أَذَاعُواْ بِهِۦۖ وَلَوۡ رَدُّوهُ إِلَى ٱلرَّسُولِ وَإِلَىٰٓ أُوْلِي ٱلۡأَمۡرِ مِنۡهُمۡ لَعَلِمَهُ ٱلَّذِينَ يَسۡتَنۢبِطُونَهُۥ مِنۡهُمۡۗ وَلَوۡلَا فَضۡلُ ٱللَّهِ عَلَيۡكُمۡ وَرَحۡمَتُهُۥ لَٱتَّبَعۡتُمُ ٱلشَّيۡطَٰنَ إِلَّا قَلِيلٗا ﴾
[النِّسَاء: 83]

Pamene iwo amva nkhani iliyonse ya mtendere kapena yochititsa mantha, iwo amaiulutsa koma iwo akanaipereka kwa Mtumwi kapena kwa amene ali ndi udindo pakati pawo kapena anthu amene amafufuza bwino nkhani, akadadziwa. Ndipo pakadapanda chisomo ndi chisoni cha Mulungu pa inu, inu mukanatsatira Satana kupatula anthu ochepa okha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا جاءهم أمر من الأمن أو الخوف أذاعوا به ولو ردوه إلى, باللغة نيانجا

﴿وإذا جاءهم أمر من الأمن أو الخوف أذاعوا به ولو ردوه إلى﴾ [النِّسَاء: 83]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo chikawadzera chinthu chilichonse chokhuza chitetezo kapena mantha, amachifalitsa. Koma akadachibwezera kwa Mtumiki ndi kwa omwe ali ndi udindo pa iwo, akadachidziwa omwe amafufuzafufuza zinthu mwa iwo (kuti kodi nzoyenera kuzifalitsa kapena ayi). Pakadapanda ubwino wa Allah ndi chifundo chake pa inu, ndithudi, mukadamtsatira satana kupatula ochepa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek