×

Motero menya nkhondo mu njira ya Mulungu, iwe siudzafunsidwa za munthu wina 4:84 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:84) ayat 84 in Chichewa

4:84 Surah An-Nisa’ ayat 84 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 84 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿فَقَٰتِلۡ فِي سَبِيلِ ٱللَّهِ لَا تُكَلَّفُ إِلَّا نَفۡسَكَۚ وَحَرِّضِ ٱلۡمُؤۡمِنِينَۖ عَسَى ٱللَّهُ أَن يَكُفَّ بَأۡسَ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْۚ وَٱللَّهُ أَشَدُّ بَأۡسٗا وَأَشَدُّ تَنكِيلٗا ﴾
[النِّسَاء: 84]

Motero menya nkhondo mu njira ya Mulungu, iwe siudzafunsidwa za munthu wina ayi koma za iwe wekha ndipo alimbikitse okhulupirira kuti mwina Mulungu adzagonjetsa anthu osakhulupirira. Mulungu ndi wamphamvu kwambiri ndi Waukali polanga

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فقاتل في سبيل الله لا تكلف إلا نفسك وحرض المؤمنين عسى الله, باللغة نيانجا

﴿فقاتل في سبيل الله لا تكلف إلا نفسك وحرض المؤمنين عسى الله﴾ [النِّسَاء: 84]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho menya nkhondo pa njira ya Allah, suukukakamizidwa (za anthu ena) koma iwe mwini, ndipo akhwirizire Asilamu. Ndithu Allah angatsekereze mtopola wa omwe sadakhulupirire. Ndipo Allah Ngwaukali kwambiri pomenya nkhondo ndiponso Wolanga kwabasi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek