Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shura ayat 46 - الشُّوري - Page - Juz 25
﴿وَمَا كَانَ لَهُم مِّنۡ أَوۡلِيَآءَ يَنصُرُونَهُم مِّن دُونِ ٱللَّهِۗ وَمَن يُضۡلِلِ ٱللَّهُ فَمَا لَهُۥ مِن سَبِيلٍ ﴾
[الشُّوري: 46]
﴿وما كان لهم من أولياء ينصرونهم من دون الله ومن يضلل الله﴾ [الشُّوري: 46]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo sadzakhala ndi athangati owapulumutsa (kuchilango cha Moto) kupatula Allah. Ndipo amene Allah wamusiya kuti asokere (chifukwa cha zochita zake zoipa) sangapeze njira (yopezera kulungama) |