Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qamar ayat 24 - القَمَر - Page - Juz 27
﴿فَقَالُوٓاْ أَبَشَرٗا مِّنَّا وَٰحِدٗا نَّتَّبِعُهُۥٓ إِنَّآ إِذٗا لَّفِي ضَلَٰلٖ وَسُعُرٍ ﴾
[القَمَر: 24]
﴿فقالوا أبشرا منا واحدا نتبعه إنا إذا لفي ضلال وسعر﴾ [القَمَر: 24]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo adati: “Kodi titsatire munthu mmodzi wochokera mwa ife? Ndithu ife ngati titamtsatira ndiye kuti tili nkusokera ndiponso misala.” |